
Amai ake Mabvuto anali amaneja a sitolo ya zovala, ndipo anali kusewenza coimilila nthawi yaitali. Nsapato zoyenela komanso kusamalila bwino miyendo yao n’kofunika kwambili kuti agwile bwino nchito yao. Posacedwapa, Mabvuto anaphunzila kufunika kwa kusamalila bwino miyendo ndiponso kadulidwe ka zikhadabu, koma amai ake sanadule bwino zikhadabu zao ndipo tsopano cala cao cinali kuwawa. Ululu unali kukulila-kulila; conco anali kufunika kupeza njila yothetsela vuto yao.
Details
- Publication Date
- Apr 23, 2022
- Language
- Chewa, Chichewa, Nyanja
- ISBN
- 9781435783089
- Category
- Children's
- Copyright
- All Rights Reserved - Standard Copyright License
- Contributors
- By (author): Trey Li
Specifications
- Pages
- 39
- Binding Type
- Paperback Perfect Bound
- Interior Color
- Color
- Dimensions
- US Trade (6 x 9 in / 152 x 229 mm)