
Cilimwe cili pafupi Mabvuto akulakalaka kupita ku chuti, koma kodi kuonekela kwa kampingambizi (kamlendo kosayembekezela) kameneka kudzasokoneza makonzedwa osangalatsa a Mabvuto ofuna kupita ku chuti? Aona kakhungu kokakala kuphazi kamene kawawa ngati ayenda; Mabvuto ali ndi kafulukutu ndipo ali ndi nkhawa kuti kangamulepheletse kupita ku chuti. Analephela kupita ku chuti caka catha cifikwa ca kudwala, nanga adzaphonyanso caka cino?
Details
- Publication Date
- Mar 22, 2022
- Language
- Chewa, Chichewa, Nyanja
- ISBN
- 9781471747915
- Category
- Children's
- Copyright
- All Rights Reserved - Standard Copyright License
- Contributors
- By (author): Trey Li
Specifications
- Pages
- 39
- Binding Type
- Paperback Perfect Bound
- Interior Color
- Color
- Dimensions
- US Trade (6 x 9 in / 152 x 229 mm)